Miyambo 26:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Mofanana ndi chitseko chimene chimangozungulira pamene anachimangirira,Waulesi nayenso amangotembenukatembenuka pabedi pake.+
14 Mofanana ndi chitseko chimene chimangozungulira pamene anachimangirira,Waulesi nayenso amangotembenukatembenuka pabedi pake.+