Miyambo 26:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Akufanana ndi munthu amene amapusitsa mnzake nʼkunena kuti, “Inetu ndimangochita zocheza.”+