Miyambo 26:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Lilime lonama limadana ndi amene lamʼpweteka,Ndipo pakamwa polankhula mwachiphamaso pamabweretsa chiwonongeko.+
28 Lilime lonama limadana ndi amene lamʼpweteka,Ndipo pakamwa polankhula mwachiphamaso pamabweretsa chiwonongeko.+