Miyambo 28:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Munthu wolemera amadziona ngati wanzeru,+Koma munthu wosauka amene ndi wozindikira amamufufuza nʼkudziwa zoona zake.+
11 Munthu wolemera amadziona ngati wanzeru,+Koma munthu wosauka amene ndi wozindikira amamufufuza nʼkudziwa zoona zake.+