Miyambo 28:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Anthu olungama zinthu zikamawayendera bwino, anthu amasangalala kwambiri,*Koma anthu oipa akayamba kulamulira, anthu amabisala.+
12 Anthu olungama zinthu zikamawayendera bwino, anthu amasangalala kwambiri,*Koma anthu oipa akayamba kulamulira, anthu amabisala.+