Miyambo 28:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Munthu amene ali ndi mlandu wa magazi chifukwa chopha munthu, adzakhala wothawathawa mpaka kumanda.*+ Aliyense asamuthandize.
17 Munthu amene ali ndi mlandu wa magazi chifukwa chopha munthu, adzakhala wothawathawa mpaka kumanda.*+ Aliyense asamuthandize.