Miyambo 28:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Wobera bambo ake ndi mayi ake nʼkumanena kuti, “Si kulakwa,”+ Amakhala ngati mnzake wa munthu wobweretsa chiwonongeko.+
24 Wobera bambo ake ndi mayi ake nʼkumanena kuti, “Si kulakwa,”+ Amakhala ngati mnzake wa munthu wobweretsa chiwonongeko.+