Miyambo 28:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Munthu wadyera amayambitsa mikangano,Koma aliyense amene amadalira Yehova zinthu zidzamuyendera bwino.*+
25 Munthu wadyera amayambitsa mikangano,Koma aliyense amene amadalira Yehova zinthu zidzamuyendera bwino.*+