Miyambo 29:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Anthu okonda kukhetsa magazi amadana ndi munthu aliyense wosalakwa,+Ndipo amafuna kuchotsa moyo wa anthu owongoka mtima.*
10 Anthu okonda kukhetsa magazi amadana ndi munthu aliyense wosalakwa,+Ndipo amafuna kuchotsa moyo wa anthu owongoka mtima.*