Miyambo 30:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Mawu onse a Mulungu ndi oyengeka.+ Iye ndi chishango kwa onse amene amathawira kwa iye.+