Miyambo 30:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Misundu* ili ndi ana aakazi awiri amene amafuula kuti, “Tipatseni! Tipatseni!” Pali zinthu zitatu zimene sizikhutaNdiponso zinthu 4 zimene sizinena kuti, “Ndakhuta!” Zinthu zake ndi izi: Miyambo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 30:15 Nsanja ya Olonda,5/15/1987, tsa. 30
15 Misundu* ili ndi ana aakazi awiri amene amafuula kuti, “Tipatseni! Tipatseni!” Pali zinthu zitatu zimene sizikhutaNdiponso zinthu 4 zimene sizinena kuti, “Ndakhuta!” Zinthu zake ndi izi: