Miyambo 31:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Nʼkosayenera kuti mafumu azimwa vinyo,Nʼkosayenera kuti mafumu azichita zimenezi, iwe Lemueli,Kapena kuti olamulira azinena kuti: “Kodi chakumwa changa chili kuti?”+ Miyambo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 31:4 Nsanja ya Olonda,2/1/2000, tsa. 30
4 Nʼkosayenera kuti mafumu azimwa vinyo,Nʼkosayenera kuti mafumu azichita zimenezi, iwe Lemueli,Kapena kuti olamulira azinena kuti: “Kodi chakumwa changa chili kuti?”+