Miyambo 31:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Amatenga ulusi ndi nsalu,Ndipo amasangalala kugwira ntchito ndi manja ake.+