Miyambo 31:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Iye amapanga zovala* nʼkuzigulitsa,Ndipo amapanga malamba nʼkuwapereka kwa amalonda.