Mlaliki 1:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Dzuwa limatuluka* ndipo dzuwa limalowa,Kenako limathamanga* kupita kumalo amene limatulukira kuti likatulukenso.+ Mlaliki Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 1:5 Kuyankha Mafunso a M’Baibulo, Mawu a Mulungu, tsa. 103
5 Dzuwa limatuluka* ndipo dzuwa limalowa,Kenako limathamanga* kupita kumalo amene limatulukira kuti likatulukenso.+