-
Mlaliki 1:10Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
10 Kodi chilipo chimene munthu anganene kuti, “Wachiona ichi, nʼchatsopanotu chimenechi?”
Ayi, chakhalapo kuyambira kalekale.
Chinalipo kale ife tisanabadwe.
-