Mlaliki 1:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Ndinatsimikiza mumtima mwanga kuti ndiphunzire ndi kufufuza mwanzeru+ zonse zimene zachitidwa padziko lapansi.+ Ndinafufuza ntchito yotopetsa kwambiri imene Mulungu wapatsa ana a anthu kuti azigwira. Mlaliki Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 1:13 Nsanja ya Olonda,2/15/1997, ptsa. 13-14
13 Ndinatsimikiza mumtima mwanga kuti ndiphunzire ndi kufufuza mwanzeru+ zonse zimene zachitidwa padziko lapansi.+ Ndinafufuza ntchito yotopetsa kwambiri imene Mulungu wapatsa ana a anthu kuti azigwira.