Mlaliki 3:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Kodi munthu wogwira ntchito amapeza phindu lanji pa ntchito yonse imene akugwira mwakhama?+