-
Mlaliki 3:18Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
18 Ndinanenanso mumtima mwanga zokhudza ana a anthu kuti Mulungu woona adzawayesa komanso kuwasonyeza kuti iwo ndi ofanana ndi nyama.
-