-
Mlaliki 4:10Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
10 Chifukwa ngati mmodzi wa iwo atagwa, winayo akhoza kuthandiza mnzakeyo kuti adzuke. Koma kodi chingachitike nʼchiyani kwa munthu amene wagwa koma palibe woti amuthandize kuti adzuke?
-