-
Mlaliki 4:15Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
15 Ndinaganizira za anthu onse amoyo amene amayenda padziko lapansi pano komanso za mmene zimakhalira ndi wachinyamata amene amalowa mʼmalo mwa mfumu.
-