Mlaliki 4:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Ngakhale kuti anthu amene ali kumbali yake ndi ambiri, anthu obwera pambuyo pake sadzasangalala naye.+ Izinso nʼzachabechabe ndipo zili ngati kuthamangitsa mphepo. Mlaliki Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 4:16 Nsanja ya Olonda,11/1/2006, tsa. 14
16 Ngakhale kuti anthu amene ali kumbali yake ndi ambiri, anthu obwera pambuyo pake sadzasangalala naye.+ Izinso nʼzachabechabe ndipo zili ngati kuthamangitsa mphepo.