Mlaliki 5:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Pali chinthu* chomvetsa chisoni kwambiri chimene ndaona padziko lapansi pano: Munthu ankangosonkhanitsa chuma koma pambuyo pake chinamupweteketsa.
13 Pali chinthu* chomvetsa chisoni kwambiri chimene ndaona padziko lapansi pano: Munthu ankangosonkhanitsa chuma koma pambuyo pake chinamupweteketsa.