-
Mlaliki 6:2Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
2 Mulungu woona amapatsa munthu chuma, katundu ndi ulemerero moti sasowa chilichonse chimene amalakalaka. Komabe Mulungu woona samulola kuti asangalale ndi zinthu zimenezi ngakhale kuti munthu wina angathe kusangalala nazo. Zimenezi nʼzachabechabe komanso tsoka lalikulu.
-