Mlaliki 6:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Ngati munthu atabereka ana 100 nʼkukhala ndi moyo zaka zambirimbiri mpaka kukalamba, koma osasangalala ndi zinthu zabwino zimene ali nazo asanalowe mʼmanda, ndithu mwana amene anabadwa wakufa ali bwino kuposa iyeyu.+
3 Ngati munthu atabereka ana 100 nʼkukhala ndi moyo zaka zambirimbiri mpaka kukalamba, koma osasangalala ndi zinthu zabwino zimene ali nazo asanalowe mʼmanda, ndithu mwana amene anabadwa wakufa ali bwino kuposa iyeyu.+