Mlaliki 6:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ntchito yonse imene munthu amagwira mwakhama amagwirira pakamwa pake,+ koma zolakalaka zake sizitha.
7 Ntchito yonse imene munthu amagwira mwakhama amagwirira pakamwa pake,+ koma zolakalaka zake sizitha.