Mlaliki 6:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Kodi pali ubwino wotani kukhala munthu wanzeru kusiyana ndi kukhala munthu wopusa?+ Kapena kodi pali phindu lanji kuti munthu wosauka amadziwa zimene angachite kuti akhale ndi moyo?*
8 Kodi pali ubwino wotani kukhala munthu wanzeru kusiyana ndi kukhala munthu wopusa?+ Kapena kodi pali phindu lanji kuti munthu wosauka amadziwa zimene angachite kuti akhale ndi moyo?*