Mlaliki 8:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Ngakhale woipa atachita zoipa maulendo 100 nʼkukhalabe ndi moyo wautali, ine ndikudziwa kuti anthu amene amaopa Mulungu woona zidzawayendera bwino, chifukwa chakuti amamuopa.+ Mlaliki Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 8:12 Nsanja ya Olonda,2/15/1997, ptsa. 17-18
12 Ngakhale woipa atachita zoipa maulendo 100 nʼkukhalabe ndi moyo wautali, ine ndikudziwa kuti anthu amene amaopa Mulungu woona zidzawayendera bwino, chifukwa chakuti amamuopa.+