Mlaliki 9:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Komanso chikondi chawo, chidani chawo ndi nsanje yawo zatha kale, ndipo alibenso gawo lililonse pa zimene zikuchitika padziko lapansi pano.+ Mlaliki Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 9:6 Nsanja ya Olonda,6/1/1995, ptsa. 6-7
6 Komanso chikondi chawo, chidani chawo ndi nsanje yawo zatha kale, ndipo alibenso gawo lililonse pa zimene zikuchitika padziko lapansi pano.+