-
Mlaliki 9:17Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
17 Ndi bwino kumvera mawu odekha a munthu wanzeru kusiyana ndi mawu ofuula a munthu amene akulamulira pakati pa anthu opusa.
-