Mlaliki 10:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Mtima wa munthu wanzeru umamutsogolera njira yoyenera,* koma mtima wa munthu wopusa umamutsogolera njira yolakwika.*+ Mlaliki Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 10:2 Nsanja ya Olonda,11/1/2006, tsa. 15
2 Mtima wa munthu wanzeru umamutsogolera njira yoyenera,* koma mtima wa munthu wopusa umamutsogolera njira yolakwika.*+