Mlaliki 10:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Zitsiru zaikidwa pamaudindo ambiri akuluakulu, koma anthu oyenerera* amangokhala pamalo otsika.