Mlaliki 11:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Iwe sudziwa mmene mzimu umachititsira kuti mafupa a mwana amene ali mʼmimba mwa mayi ake akule.+ Mofanana ndi zimenezi sudziwanso ntchito ya Mulungu woona, amene amachita zinthu zonse.+
5 Iwe sudziwa mmene mzimu umachititsira kuti mafupa a mwana amene ali mʼmimba mwa mayi ake akule.+ Mofanana ndi zimenezi sudziwanso ntchito ya Mulungu woona, amene amachita zinthu zonse.+