Mlaliki 11:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ngati munthu atakhala ndi moyo zaka zambiri, azisangalala pa zaka zonsezo.+ Koma azikumbukira kuti masiku a mdima akhoza kukhala ambiri. Zonse zimene zikubwera nʼzachabechabe.+ Mlaliki Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 11:8 Nsanja ya Olonda,11/1/2006, tsa. 158/15/1998, tsa. 9
8 Ngati munthu atakhala ndi moyo zaka zambiri, azisangalala pa zaka zonsezo.+ Koma azikumbukira kuti masiku a mdima akhoza kukhala ambiri. Zonse zimene zikubwera nʼzachabechabe.+