-
Nyimbo ya Solomo 1:8Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
8 “Ngati iweyo sukudziwa, iwe mkazi wokongola kwambiri kuposa akazi onse,
Tsatira mapazi a ziweto
Ndipo ukadyetse mbuzi zako zingʼonozingʼono pafupi ndi matenti a abusa.”
-