Nyimbo ya Solomo 1:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 “Ndiwe wokongola wokondedwa wanga. Ndiwe chiphadzuwa. Maso ako ali ngati maso a njiwa.”+ Nyimbo ya Solomo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 1:15 Nsanja ya Olonda,11/15/2006, tsa. 18