-
Nyimbo ya Solomo 2:3Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
3 “Mofanana ndi mtengo wa maapozi pakati pa mitengo yamʼnkhalango,
Ndi mmene alili wachikondi wanga pakati pa ana aamuna.
Ndikulakalaka kwambiri nditakhala pansi pamthunzi wa wokondedwa wanga.
Ndipo chipatso chake ndi chotsekemera.
-