-
Nyimbo ya Solomo 2:8Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
8 Ndikumva wachikondi wanga akubwera.
Taonani! Uyo akubwera apoyo,
Akukwera mapiri ndipo akudumpha zitunda.
-