Nyimbo ya Solomo 2:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Wachikondi wanga ali ngati insa komanso mphoyo yaingʼono.+ Taonani! Iye waima kuseri kwa khoma la nyumba yathu.Akuyangʼana mʼmawindo,Akusuzumira pazotchingira mʼmawindo.
9 Wachikondi wanga ali ngati insa komanso mphoyo yaingʼono.+ Taonani! Iye waima kuseri kwa khoma la nyumba yathu.Akuyangʼana mʼmawindo,Akusuzumira pazotchingira mʼmawindo.