-
Nyimbo ya Solomo 3:8Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
8 Onsewo atenga malupanga,
Ndipo onse ndi ophunzitsidwa nkhondo,
Aliyense wamangirira lupanga lake mʼchiuno
Kuti adziteteze ku zinthu zoopsa za usiku.”
-