Nyimbo ya Solomo 3:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 “Tulukani, inu ana aakazi a Ziyoni,Pitani mukaone Mfumu SolomoItavala nkhata yamaluwa, imene mayi ake+ anailukiraKuti ivale pa tsiku la ukwati wake,Pa tsiku limene mtima wa mfumuyo unasangalala.”
11 “Tulukani, inu ana aakazi a Ziyoni,Pitani mukaone Mfumu SolomoItavala nkhata yamaluwa, imene mayi ake+ anailukiraKuti ivale pa tsiku la ukwati wake,Pa tsiku limene mtima wa mfumuyo unasangalala.”