Nyimbo ya Solomo 4:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Watenga mtima wanga,+ iwe mchemwali wanga, mkwatibwi wanga,Watenga mtima wanga utangondiyangʼana kamodzi kokha,Ndiponso ndi mkanda wa mʼkhosi mwako.
9 Watenga mtima wanga,+ iwe mchemwali wanga, mkwatibwi wanga,Watenga mtima wanga utangondiyangʼana kamodzi kokha,Ndiponso ndi mkanda wa mʼkhosi mwako.