Nyimbo ya Solomo 4:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Uli ngati kasupe wamʼmunda, chitsime chamadzi abwino,Ndiponso timitsinje tochokera ku Lebanoni.+