Nyimbo ya Solomo 5:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ndinamʼtsegulira wachikondi wanga,Koma wachikondi wangayo anali atachokapo, atapita. Ndinadandaula kwambiri atachoka. Ndinamufunafuna koma sindinamupeze.+ Ndinamuitana koma sanandiyankhe.
6 Ndinamʼtsegulira wachikondi wanga,Koma wachikondi wangayo anali atachokapo, atapita. Ndinadandaula kwambiri atachoka. Ndinamufunafuna koma sindinamupeze.+ Ndinamuitana koma sanandiyankhe.