Nyimbo ya Solomo 5:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Alonda amene ankazungulira mumzinda anandipeza. Anandimenya ndipo anandivulaza. Alonda apamipanda anandilanda chofunda changa.*
7 Alonda amene ankazungulira mumzinda anandipeza. Anandimenya ndipo anandivulaza. Alonda apamipanda anandilanda chofunda changa.*