-
Nyimbo ya Solomo 5:9Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
9 “Kodi wachikondi wakoyo akuposa bwanji achikondi ena onse,
Iwe mkazi wokongola kwambiri kuposa akazi onse?
Kodi wachikondi wakoyo akuposa bwanji achikondi ena onse,
Kuti utilumbiritse lumbiro limeneli?”
-