Nyimbo ya Solomo 5:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Mutu wake ndi wokongola ngati golide, golide wabwino kwambiri. Tsitsi lake lopotanapotana lili ngati nthambi za kanjedza* zimene zikugwedera,Ndipo ndi lakuda ngati khwangwala.
11 Mutu wake ndi wokongola ngati golide, golide wabwino kwambiri. Tsitsi lake lopotanapotana lili ngati nthambi za kanjedza* zimene zikugwedera,Ndipo ndi lakuda ngati khwangwala.