Nyimbo ya Solomo 5:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Masaya ake ali ngati bedi la maluwa onunkhira,+Ndiponso ngati munda wa zitsamba zonunkhira umene uli pamalo okwera. Milomo yake ili ngati maluwa amene akuchucha mafuta a mule.+
13 Masaya ake ali ngati bedi la maluwa onunkhira,+Ndiponso ngati munda wa zitsamba zonunkhira umene uli pamalo okwera. Milomo yake ili ngati maluwa amene akuchucha mafuta a mule.+