Nyimbo ya Solomo 5:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Miyendo yake ili ngati zipilala zamiyala ya mabo zozikidwa pazitsulo zagolide wabwino kwambiri. Iye ndi wokongola ngati dziko la Lebanoni ndipo ndi wamtali mofanana ndi mitengo ya mkungudza.+ Nyimbo ya Solomo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 5:15 Nsanja ya Olonda,11/15/2006, tsa. 19
15 Miyendo yake ili ngati zipilala zamiyala ya mabo zozikidwa pazitsulo zagolide wabwino kwambiri. Iye ndi wokongola ngati dziko la Lebanoni ndipo ndi wamtali mofanana ndi mitengo ya mkungudza.+