-
Nyimbo ya Solomo 6:6Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
6 Mano ako ali ngati gulu la nkhosa
Zimene zikuchokera kosambitsidwa,
Zonse zabereka mapasa,
Ndipo palibe imene ana ake afa.
-